Psalms 55:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Mulungu, mulole kuti imfa iŵagwere adani anga, atsikire ku manda akadali moyo, pakuti zoipa zili tho m'mitima ndi m'nyumba zao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Imfa iwagwere modzidzimutsa, atsikire kumanda ali amoyo, pakuti m'mokhala mwao muli zoipa pakati pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulole imfa itenge adani anga mwadzidzidzi; alowe mʼmanda ali amoyo pakuti choyipa chili pakati pawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Imfa iwagwere modzidzimutsa, Atsikire kumanda ali amoyo: Pakuti m'mokhala mwao muli zoipa pakati pao,