Psalms 55:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Madzulo, m'maŵa ndi masana ndikudandaula ndi kulira, ndipo Iye adzamva mau anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Madzulo, m'mawa, ndi msana ndidzadandaula, ndi kubuula, ndipo adzamva mau anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Madzulo, mmawa ndi masana ndimalira mowawidwa mtima, ndipo Iye amamva mawu anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Madzulo, m'mawa, ndi msana ndidzadandaula, ndi kubuula, Ndipo adzamva mau anga.