Psalms 55:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzapulumutsa moyo wanga pa nkhondo imene ndikumenya, pakuti anthu ambiri akukangana nane.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anaombola moyo wanga kunkhondo yondilaka, ndikhale mumtendere, pakuti ndiwo ambiri okangana nane.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amandiwombola ine osavulazidwa pa nkhondo imene yafika kulimbana nane, ngakhale kuti ndi ambiri amene akunditsutsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anaombola moyo wanga ku nkhondo yondilaka, ndikhale mumtendere: Pakuti ndiwo ambiri okangana nane.