Psalms 55:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtima wanga ukumva ululu woopsa, zoopsa za imfa zandigwera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mtima wanga uwawa m'kati mwanga; ndipo zoopsa za imfa zandigwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtima wanga ukupweteka mʼkati mwanga; mantha a imfa andigwera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mtima wanga uwawa m'kati mwanga; Ndipo zoopsa za imfa zandigwera.