Psalms 55:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo ndimati, “Ndikadakhala ndi mapiko onga a njiŵa, bwenzi nditauluka kupita kutali kukapuma.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinati, Ha, wina akadandipatsa mapiko onga a njiwa! Mwenzi nditauluka, ndi kukhaliratu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinati, “Ndithu, ndikanakhala ndi mapiko ankhunda! Ndikanawulukira kutali ndi kukapuma.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinati, Ha, wina akadandipatsa mapiko onga a njiwa Mwenzi nditauluka, ndi kukhaliratu.