Psalms 55:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Ambuye, onongani zolinga za adani anga, musokoneze upo wao. Pakuti ndikuwona anthu akuchita chiwawa ndi nkhondo mumzindamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Aonongeni, Ambuye, gawani lilime lao, pakuti ndaona chiwawa ndi ndeu m'mudzimo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sokonezani maganizo a oyipa, Inu Ambuye, tsutsani mawu awo; pakuti ine ndikuona chiwawa ndi mkangano mu mzinda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Aonongeni, Ambuye, gawani lilime lao: Pakuti ndaona ciwawa ndi ndeu m'mudzimo.