Psalms 56:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti mwalanditsa moyo wanga ku imfa. Inde mwandichirikiza mapazi kuti ndisagwe, kuti motero ndiziyenda pamaso pa Mulungu m'kuŵala kwa amoyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mwalanditsa moyo wanga kuimfa, simunatero nao mapazi anga kuti ndingagwe? Kuti ndiyende pamaso pa Mulungu m'kuunika kwa amoyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti mwawombola moyo wanga ku imfa ndi mapazi anga kuti ndingagwe, kuti ndiyende pamaso pa Mulungu mʼkuwala kwa moyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mwalanditsa moyo wanga kuimfa: Simunatero nao mapazi anga kuti ndingagwe? Kuti ndiyende pamaso pa Mulungu M'kuunika kwa amoyo.