Psalms 56:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amasonkhana okhaokha namabisalira, amalonda mayendedwe anga, amafuna kundipha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amemezana, alalira, atchereza mapazi anga, popeza alindira moyo wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amakambirana, amandibisalira, amayangʼanitsitsa mayendedwe anga ndipo amakhala ndi chidwi chofuna kuchotsa moyo wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amemezana, alalira, Achereza mapazi anga, Popeza alindira moyo wanga.