Psalms 56:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muŵalange chifukwa cha zoipa zao. Inu Mulungu, muŵakwiyire anthuwo ndi kuŵaononga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi adzapulumuka ndi zopanda pake? Gwetsani anthu mumkwiyo, Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musalole konse kuti athawe; mu mkwiyo wanu Mulungu mugwetse mitundu ya anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi adzapulumuka ndi zopanda pace? Gwetsani anthu mumkwiyo, Mulungu.