Psalms 56:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adani anga adzabwezedwa m'mbuyo pa tsiku lomwe ndidzaitana Mulungu. Ndikudziŵa kuti Mulungu ali pa mbali yanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo adani anga adzabwerera m'mbuyo tsiku lakuitana ine. Ichi ndidziwa, kuti Mulungu avomerezana nane.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Adani anga adzabwerera mʼmbuyo pamene ndidzalirira kwa Inu. Pamenepo ndidzadziwa kuti Mulungu ali ku mbali yanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo adani anga adzabwerera m'mbuyo tsiku lakuitana ine: Ici ndidziwa, kuti Mulungu abvomerezana nane.