Psalms 57:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pakuti chikondi chanu chosasinthika nchachikulu, chofika mpaka mlengalenga, kukhulupirika kwanu kumafika mpaka ku mitambo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti chifundo chanu nchachikulu kufikira m'mwamba, ndi choonadi chanu kufikira mitambo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti chikondi chanu nʼchachikulu, kufikira ku mayiko akumwamba; kukhulupirika kwanu kwafika ku mitambo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti cifundo canu ncacikuru kufikira m'mwamba, Ndi coonadi canu kufikira mitambo.