Psalms 57:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu adzandiyankha ali kumwamba, ndipo adzandipulumutsa. Iye adzasokoneza amene andipondereza. Adzaonetsa chikondi chake chosasinthika, adzaonetsa kukhulupirika kwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzanditumizira m'mwamba, nadzandipulumutsa ponditonza wofuna kundimeza; Mulungu adzatumiza chifundo chake ndi choonadi chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu amanditumizira kuchokera kumwamba ndi kundipulumutsa, kudzudzula iwo amene akundithamangitsa kwambiri. Mulungu amatumiza chikondi chake ndi kukhulupirika kwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzanditumizira m'mwamba, nadzandipulumutsa Ponditonza wofuna kundimeza; Mulungu adzatumiza cifundo cace ndi coonadi cace.