Psalms 57:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndimagona pakati pa anthu olusa amene ali ngati mikango. Mano ao ali ngati mikondo ndi mivi, lilime lao lili ngati lupanga lakuthwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Moyo wanga uli pakati pa mikango; ndigona pakati pa oyaka moto, ndiwo ana a anthu amene mano ao ali nthungo ndi mivi, ndipo lilime lao ndilo lupanga lakuthawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndili pakati pa mikango, ndagona pakati pa zirombo zolusa; anthu amene mano awo ndi milomo yawo ndi mivi, malilime awo ndi malupanga akuthwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Moyo wanga uli pakati pa mikango; Ndigona pakati pa oyaka moto, Ndiwo ana a anthu amene mano ao ali nthungo ndi mibvi, Ndipo lilime lao ndilio lupanga lakuthwa.