Psalms 57:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Mulungu, mtima wanga wakonzeka, ndithu mtima wanga wakonzekadi. Ndidzaimba nyimbo, nyimbo yake yotamanda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mtima wanga wakhazikika, Mulungu, ndakhazika mtima; ndidzaimba, inde, ndidzaimba zolemekeza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtima wanga ndi wokhazikika, Inu Mulungu mtima wanga ndi wokhazikika. Ndidzayimba nyimbo, nyimbo yake yamatamando.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mtima wanga wakhazikika, Mulungu, ndakhazika mtima; Ndidzayimba, inde, ndidzayimba zolemekeza.