Psalms 57:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Lumpha iwe mtima wanga. Inu zeze ndi pangwe, tiyeni lirani, Ndidzadzutsa dzuŵa ndi nyimbo zanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Galamuka, ulemu wanga; galamukani chisakasa ndi zeze! Ndidzauka ndekha mamawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzuka moyo wanga! Dzukani zeze ndi pangwe! Ndidzadzuka mʼbandakucha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Galamuka, ulemu wanga; galamukani cisakasa ndi zeze: Ndidzauka ndekha mamawa.