Psalms 57:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakuthokozani, Inu Chauta, pakati pa mitundu ya anthu. Ndidzaimba nyimbo zokutamandani pakati pa anthu a maiko onse,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzakuyamikirani mwa anthu, Ambuye, ndidzakuimbirani mwa mitundu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakutamandani Ambuye, pakati pa mitundu ya anthu, ndidzayimba za Inu pakati pa mayiko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzakuyamikirani mwa anthu, Ambuye: Ndidzakuyimbirani mwa mitundu.