Psalms 58:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wangwiro adzakondwera poona kulipsirako. Adzasamba mapazi ake m'magazi a anthu oipawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wolungama adzakondwera pakuona kubwezera chilango, adzasamba mapazi ake m'mwazi wa woipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Olungama adzasangalala poona kubwezera chilango, pamene adzasambitsa mapazi awo mʼmagazi a anthu oyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wolungama adzakondwera pakuona kubwezera cilango: Adzasamba mapazi ace m'mwazi wa woipa.