Psalms 58:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero anthu adzati, “Zoona, olungama amalandiradi mphotho. Alipodi Mulungu amene amaweruza pa dziko lapansi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu adzati, Indedi, pali mphotho kwa wolungama. Indedi, pali Mulungu wakuweruza pa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anthu adzanena kuti, “Zoonadi, olungama amalandirabe mphotho; zoonadi kuli Mulungu amene amaweruza dziko lapansi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu adzati, Indedi, pali mphotho kwa wolungama; Indedi, pali Mulungu wakuweruza pa dziko lapansi.