Psalms 58:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iyai, mitima yanu imangolingalira zoipa, kuweruza kwanu kosalungama kumadzetsa chiwawa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inde, mumtima muchita zosalungama; pa dziko lapansi mugawira anthu chiwawa cha m'manja mwanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ayi, mʼmitima mwanu mumakonzekera zosalungama, ndipo manja anu amatulutsa zachiwawa pa dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inde, mumtima mucita zosalungama; Pa dziko lapansi mugawira anthu ciwawa ca m'manja mwanu.