Psalms 58:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ali ndi ululu wonga wa njoka, ali ngati mphiri yogontha, imene yatseka makutu ake,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ululu wao ukunga wa njoka; akunga mphiri yogontha m'khutu, itseka m'khutu mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ululu wawo uli ngati ululu wa njoka, ngati uja wa mphiri imene yatseka mʼmakutu mwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ululu wao ukunga wa njoka; Akunga mphiri yogontha m'khutu, itseka m'khutu mwace.