Psalms 58:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Mulungu, gululani mano a m'kamwa mwao, phwanyani nsagwada za mikangoyi, Inu Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Thyolani mano ao m'kamwa mwao, Mulungu, zulani zitsakano za misona ya mkango, Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gululani mano mʼkamwa mwawo, Inu Mulungu, Yehova khadzulani mano a mikango!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tyolani mano ao m'kamwa mwao, Mulungu: Zulani zitsakano za misona ya mkango, Yehova.