Psalms 58:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Azimirire ngati madzi opita, mivi yao iŵafotere m'manja ngati udzu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Apitetu ngati madzi oyenda; popiringidza mivi yake ikhale yodukaduka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulole kuti asowe ngati madzi oyenda pamene iwo akoka uta mulole kuti mivi yawo ikhale yosathwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Apitetu ngati madzi oyenda; Popiringidza mibvi yace ikhale yodukaduka.