Psalms 58:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akhale ngati nkhonodambe imene imazimirira poyenda, ngati mtayo wosaona dzuŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Apite ngati nkhono yosungunuka; asaone dzuwa monga mtayo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akhale ngati nkhono imene imasungunuka pamene ikuyenda; ngati mwana wakufa asanabadwe, iwo asaone dzuwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Apite ngati nkhono yosungunuka; Asaone dzuwa monga mtayo,