Psalms 58:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Miphika yanu isanagwire moto wa nkhuni zaminga, zingakhale zaziŵisi kapena zoyaka, Mulungu aziseseretu nkuzichotsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Miphika yanu isanagwire moto waminga, adzaiuluza, yaiwisi ndi yoyaka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Miphika yanu isanagwire moto waminga ya mkandankhuku, kaya iyo ndi yobiriwira kapena yowuma, oyipa adzachotsedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Miphika yanu isanagwire moto waminga, Adzaiuluza, yaiwisi ndi yoyaka.