Psalms 59:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pulumutseni kwa adani anga, Inu Mulungu wanga, tetezeni kwa anthu ondiwukira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Altasheti. Mikitamu wa Davide. Muja Saulo anatuma anthu adikire nyumba yake, kuti amuphe. Ndilanditseni kwa adani anga, Mulungu wanga, ndiikeni pamsanje kwa iwo akundiukira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Potsata mayimbidwe a “Musawononge.” Ndakatulo ya Davide. Pamene Sauli anatumiza anthu kuti akalondere nyumba ya Davide ndi cholinga choti amuphe. Landitseni kwa adani anga, Inu Mulungu; munditeteze kwa anthu amene auka kutsutsana nane.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndilanditseni kwa adani anga, Mulungu wanga: Ndiikeni pamsanje kwa iwo akundiukira.