Psalms 59:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu wanga adzandichingamira chifukwa ndi wa chikondi chosasinthika. Mulungu wanga adzandilola kuti ndisangalale poona adani anga atagonja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu wa chifundo changa adzandichingamira, adzandionetsa tsoka la adani anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu wanga wachikondi. Mulungu adzapita patsogolo panga ndipo adzandilola kunyada pa iwo amene amandinyoza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu wa cifundo canga adzandikumika: Adzandionetsa tsoka la adani anga.