Psalms 59:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musaŵaphe pomwepa, kuwopa kuti anthu anga angaiŵale, koma muŵabalalitse ndi mphamvu zanu, ndipo muŵagwetse, Inu Ambuye, Inu chishango changa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musawapheretu, angaiwale anthu anga, muwabalalitse mwa mphamvu yanu, ndipo muwagwetse, Ambuye, ndinu chikopa chathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma musawaphe, Inu Ambuye chishango chathu, kuopa kuti anthu anga angayiwale. Mwa mphamvu zanu, lolani kuti azingoyendayenda ndipo muwatsitse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musawapheretu, angaiwale anthu anga: Muwabalalitse mwa mphamvu yanu, ndipo muwagwetse, Ambuye, ndinu cikopa cathu.