Psalms 59:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akodwe ndi kunyada kwao, chifukwa cha uchimo wa m'kamwa mwao, ndi mau a pakamwa pao. Chifukwa chakuti amatemberera ndipo amanama,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakamwa pao achimwa ndi mau onse a pa milomo yao, potero akodwe m'kudzitamandira kwao, ndiponso chifukwa cha kutemberera ndi bodza azilankhula.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa cha machimo a pakamwa pawo chifukwa cha mawu a milomo yawo, iwo akodwe mʼkunyada kwawo. Chifukwa cha matemberero ndi mabodza amene ayankhula
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakamwa pao acimwa ndi mau onse a pa milomo yao, Potero akodwe m'kudzitamandira kwao, Ndiponso cifukwa ca kutemberera ndi bodza azilankhula.