Psalms 59:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onani, iwo akubisalira moyo wanga, anthu oopsa agwirizana kuti andithire nkhondo. Ngakhale sindidachite choipa kapena kuchimwa konse, Inu Chauta,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti onani, alalira moyo wanga; amphamvu andipangira chiwembu, osachimwa, osalakwa ine, Yehova,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onani momwe iwo akundibisalira! Anthu owopsa agwirizana zolimbana nane; osati chifukwa cha mlandu kapena tchimo langa, Inu Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti onani, alalira moyo wanga; Amphamvu andipangira ciwembu: Osacimwa, osalakwa ine, Yehova,