Psalms 59:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ngakhale sindidalakwe, anthuwo akuthamanga kukonzekera nkhondo. Dzambatukani, mudzandithandize, ndipo muwone.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
osawapatsa chifukwa ine, athamanga nadzikonza. Galamukani kukomana nane, ndipo penyani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine sindinachite cholakwa, koma iwo ndi okonzeka kundithira nkhondo. Dzukani kuti mundithandize; penyani mavuto anga!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Osawapatsa cifukwa ine, athamanga nadzikonza; Galamukani kukomana nane, ndipo penyani.