Psalms 59:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Awo ali ukowo, akulongolola kwambiri, ndipo akufuula mwankhalwe, chifukwa m'maganizo mwao amati, “Ndani akutimva nanga?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Onani abwetuka pakamwa pao; m'milomo mwao muli lupanga, pakuti amati, Amva ndani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onani zomwe amalavula mʼkamwa mwawo; iwo amalavula malupanga kuchokera pa milomo yawo, ndipo amanena kuti, “Ndani angatimve?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Onani abwetuka pakamwa pao; M'milomo mwao muli lupanga, Pakuti amati, Amva ndani?