Psalms 59:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Inu Chauta, mumangoŵaseka. Inu mumanyozera anthu onse akunja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Inu, Yehova, mudzawaseka; mudzalalatira amitundu onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Inu Yehova, mumawaseka, mumayinyoza mitundu yonseyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Inu, Yehova, mudzawaseka; Mudzalalatira amitundu onse.