Psalms 6:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtima wanganso wazunzika kwambiri. Nanga Inu Chauta, zimenezi zidzakhala zikuchitika mpaka liti?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Moyo wanganso wanthunthumira kwakukulu; ndipo Inu, Yehova, kufikira liti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Moyo wanga uli pa mazunzo aakulu. Mpaka liti, Inu Yehova, mpaka liti?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Moyo wanganso wanthunthumira kwakukuru; Ndipo Inu, Yehova, kufikira liti?