Psalms 6:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu akufa sangathe kukutamandani ku manda. M'dziko la akufa ndani angathe kukuyamikani?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti muimfa m'mosakumbukira Inu; m'mandamo adzakuyamikani ndani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Palibe amene amakukumbukirani pamene wamwalira; Amakutamandani ndani ali ku manda?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti muimfa m'mosakumbukila Inu: M'mandamo adzakuyamikani dani?