Psalms 6:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maso anga atupa chifukwa cha kulira, afooka chifukwa cha adani anga onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Lapuwala diso langa chifukwa cha chisoni; lakalamba chifukwa cha onse akundisautsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Maso anga atupa chifukwa cha chisoni; akulephera kuona chifukwa cha adani anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Lapuwala diso langa cifukwa ca cisoni; Lakalamba cifukwa ca onse akundisautsa.