Psalms 6:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chokani apa, inu nonse ochita zoipa, Chauta wamva kulira kwanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chokani kwa ine, nonsenu akuchita zopanda pake; pakuti wamva Yehova mau a kulira kwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chokani kwa ine inu nonse amene mumachita zoyipa, pakuti Yehova wamva kulira kwanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cokani kwa ine, nonsenu akucita zopanda pace; Pakuti wamva Yehova mau a kulira kwanaa,