Psalms 60:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mwagwedeza dziko ndi chivomezi, Inu mwaling'amba. Konzani ming'alu yake, pakuti likugwedezeka koopsa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwagwedeza dziko, mwaling'amba. Konzani ming'alu yake; pakuti ligwedezeka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mwagwedeza dziko ndipo mwalingʼamba, konzani mingʼalu yake pakuti ikugwedezeka kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwagwedeza dziko, mwaling'amba: Konzani ming'alu yace; pakuti ligwedezeka.