Psalms 60:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mwalola anthu anu kuti aone mavuto aakulu. Mwatipatsa vinyo wachilango kuti timwe, ndipo tikudzandira naye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwaonetsa anthu anu zowawa, mwatimwetsa vinyo wotinjenjemeretsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mwaonetsa anthu anu nthawi za mavuto; inu mwatipatsa vinyo amene watichititsa kudzandira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwaonetsa anthu anu zowawa: Mwatimwetsa vinyo wotinjenjemeretsa.