Psalms 60:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe Inu mwatikwezera mbendera ife amene timakuwopani, kuti tisonkhanireko pothaŵa uta wankhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mwapatsa mbendera akuopa Inu, aikweze chifukwa cha choonadi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma kwa iwo amene amaopa Inu, Inu mwakweza mbendera kuti tisonkhanireko pothawa uta.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mwapatsa mbendera akuopa Inu, Aikweze cifukwa ca coonadi.