Psalms 60:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Giliyadi ndi wanga, Manase ndi wanga. Efuremu ali ngati chisoti changa chodzitetezera, Yuda ali ngati ndodo yanga yaufumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Giliyadi ndi wanga, Manasenso ndi wanga; ndipo Efuremu ndi mphamvu ya mutu wanga; Yuda ndiye wolamulira wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Giliyadi ndi wanga, Manase ndi wanganso; Efereimu ndi chipewa changa chodzitetezera, Yuda ndi ndodo yanga yaufumu
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Gileadi ndi wanga, Manasenso ndi wanga; Ndipo Efraimu ndi mphamvu ya mutu wanga; Yuda ndiye wolamulira wanga,