Psalms 61:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inutu ndinu kothaŵira kwanga, nsanja yolimba yonditeteza kwa adani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti munakhala pothawirapo panga; nsanja yolimba pothawa mdani ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Inu mwakhala pothawirapo panga, nsanja yolimba polimbana ndi adani anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti munakhala pothawirapo panga; nsanja yolimba pathawa mdani ine.