Psalms 61:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akhale pa mpando wake waufumu pamaso pa Mulungu mpaka muyaya. Inu Chauta, mumsunge mokhulupirika chifukwa cha chikondi chanu chosasinthika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzakhala nthawi zonse pamaso pa Mulungu; mumpatse chifundo ndi choonadi zimsunge.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye akhale pa mpando waufumu pamaso pa Mulungu kwamuyaya; ikani chikondi chanu ndi kukhulupirika kwanu kuti zimuteteze.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzakhala nthawi zonse pamaso pa Mulungu; Mumpatse cifundo ndi coonadi zimsunge.