Psalms 62:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtima wanga umakhala chete kuyembekezera Mulungu yekha, pakuti chipulumutso changa chimafumira kwa Iye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Mkulu wa Nyimbo, pa Yedutuni, Salimo la Davide. Moyo wanga ukhalira chete Mulungu yekha; chipulumutso changa chifuma kwa Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Kutsata mayimbidwe a Yedutuni. Salimo la Davide. Moyo wanga umapeza mpumulo mwa Mulungu yekha; chipulumutso changa chimachokera kwa Iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Moyo wanga ukhalira cete Mulungu yekha: Cipulumutso canga cifuma kwa Iye.