Psalms 62:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu adalankhula kamodzi, ine ndaphunzirapo zinthu ziŵiri, china ndi chakuti mphamvu ndi zanu, Inu Mulungu,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu ananena kamodzi, ndinachimva kawiri, kuti mphamvu ndi yake ya Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu wayankhula kamodzi, ine ndamvapo zinthu ziwiri; choyamba nʼchakuti Inu Mulungu ndinu wamphamvu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu ananena kamodzi, ndinacimva kawiri: Kuti mphamvu ndi yace ya Mulungu: