Psalms 62:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
chikondi chanu nchosasinthika, Inu Ambuye; china ndi chakuti Inu mumabwezera munthu molingana ndi ntchito zake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifundonso ndi chanu, Ambuye, Chifukwa Inu mubwezera munthu aliyense monga mwa ntchito yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
komanso Inu Ambuye, chikondi chanu nʼchosasinthika. Chachiwiri nʼchakuti mumamuchitira munthu molingana ndi ntchito zake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifundonso ndi canu, Ambuye: Cifukwa Inu musudzula munthu ali yense monga mwa nchito yace.