Psalms 62:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu otsika ndi mpweya chabe, ngakhale anthu okwera ndi nthunzi chabe, onsewo ndi oluluka pa sikelo, ndi opepuka kupambana mpweya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Indetu, anthu achabe ndi mpweya, ndipo anthu akulu ndi bodza, pakuwayesa apepuka; onse pamodzi apepuka koposa mpweya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu wamba ndi mpweya chabe; anthu apamwamba ndi bodza chabe; ngati atayezedwa pa sikelo iwo ndi chabe; iwowo pamodzi ndi mpweya ndi chabe
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Indetu, anthu acabe ndi mpweya, ndipo anthu akuru ndi bodza: Pakuwayesa apepuka; Onse pamodzi apepuka koposa mpweya,