Psalms 63:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo adzaperekedwa kuti akaphedwe ku nkhondo, motero adzasanduka chakudya cha nkhandwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzawapereka kumphamvu ya lupanga; iwo adzakhala gawo la ankhandwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo adzaperekedwa ku lupanga ndi kukhala chakudya cha ankhandwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzawapereka ku mphamvu ya lupanga; Iwo adzakhala gawo la ankhandwe.