Psalms 63:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mfumu idzakondwera mwa Mulungu. Onse olumbirira Iye, adzamtamanda, koma pakamwa pa anthu abodza padzatsekedwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mfumu idzakondwera mwa Mulungu; yense wakulumbirira iye adzatamandira; pakuti pakamwa pa iwo onena bodza padzatsekedwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mfumu idzakondwera mwa Mulungu; onse amene amalumbira mʼdzina la Mulungu adzalemekeza Mulunguyo, koma pakamwa pa anthu onama padzatsekedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mfumu idzakondwera mwa Mulungu; Yense wakulumbirira iye adzatamandira; Pakuti pakamwa pa iwo onena bodza padzatsekedwa.