Psalms 63:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikukhumbira kukuwonani m'malo anu oyera ndi kuwona mphamvu zanu ndi ulemerero wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuti ndione mphamvu yanu ndi ulemerero wanu, monga ndinakuonani m'malo oyera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu ndinakuonani ku malo anu opatulika ndipo ndinapenya mphamvu zanu ndi ulemerero wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti ndione mphamvu yanu ndi ulemerero wanu, Monga ndinakuonani m'malo oyera.