Psalms 63:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho ndidzakutamandani masiku onse a moyo wanga. Ndidzakweza manja anga kwa Inu mopemphera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero ndidzakuyamikani m'moyo mwanga; ndidzakweza manja anga m'dzina lanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakutamandani masiku onse a moyo wanga, ndipo mʼdzina lanu ndidzakweza manja anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero ndidzakuyamikani m'moyo mwanga; Ndidzakweza manja anga m'dzina lanu.